Yohane 4:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo mkazi wa m'Samariya ananena ndi iye, Bwanji Inu, muli Myuda, mupempha kwa ine kumwa, ndine mkazi Msamariya? (pakuti Ayuda sayenderana nao Asamariya),

Yohane 4

Yohane 4:7-18