Yohane 4:53 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace atateyo anadziwa kuti ndi ora lomwelo limene Yesu anati kwa iye, Mwana wako ali ndi moyo; ndipo anakhulupira iye yekha ndi a pa banja lace onse.

Yohane 4

Yohane 4:48-54