Yohane 4:42 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ananena kwa mkazi, kuti, Tsopano sitikhulupira cifukwa ca kulankhula kwako: pakuti tamva tokha, ndipo tidziwa kuti Mpulumutsi wa dziko lapansi ndi Iyeyu ndithu.

Yohane 4

Yohane 4:35-51