Yohane 4:11-13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

11. Mkaziyo ananena ndi Iye, Ambuye, mulibe cotungira madzi, ndi citsime ciri cakuya; ndipo mwatenga kuti madzi amoyo?

12. kodi muli wamkuru ndi atate wathu Yakobo amene anatipatsa ife citsimeci, namwamo iye yekha, ndi ana ace, ndi zoweta zace?

13. Yesu anayankha nati kwa iye, Yense wakumwako madzi awa adzamvanso Iudzu;

Yohane 4