Yohane 3:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wokhulupirira Iye saweruzidwa; wosakhulupira waweruzidwa ngakhale tsopano, cifukwa sanakhulupirira dzina la Mwana wobadwa yekha wa Mulungu.

Yohane 3

Yohane 3:9-27