Yohane 21:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma anati kwa iwo, Ponyani khoka ku mbali ya dzanja lamanja ya ngalawa, ndipo mudzapeza, Pamenepo anaponya, ndipo analibenso mphamvu yakulikoka cifukwa ca kucuruka nsomba.

Yohane 21

Yohane 21:3-12