Yohane 21:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ananena nayenso kaciwiri, Simoni mwana wa Yona, ukonda Ine kodi? Ananena ndi iye, Inde, Ambuye; mudziwa kuti ndikukondani Inu. Ananena naye, Weta nkhosa zanga.

Yohane 21

Yohane 21:6-25