Yohane 20:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakupita masiku asanu ndi atatu akuphunzira ace analinso m'nyumbamo, ndi Tomasi pamodzi nao: Yesu anadza, makomo ali citsekere, naimirira pakati, nati, Mtendere ukhale ndi inu.

Yohane 20

Yohane 20:24-31