Yohane 2:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace atauka kwa akufa, akuphunzira ace anakumbukira kuti ananena ici; ndipo anakhulupirira colemba, ndi mau amene Yesu ananena.

Yohane 2

Yohane 2:18-25