Yohane 19:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace Pilato ananena kwa iye, Simulankhula ndi ine kodi? simudziwa kodi kuti ulamuliro ndiri nao wakukumasulani, ndipo ndiri nao ulamuliro wakukupacikani?

Yohane 19

Yohane 19:5-14