Yohane 19:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Pamenepo tsono Pilato anatenga Yesu, namkwapula.

2. Ndipo asilikari, m'mene analuka korona waminga anambveka pamutu pace, nampfunda iye maraya acibakuwa;

3. nadza kwa iye, nanena, Tikuoneni, Mfumu ya Ayuda! nampanda khofu.

Yohane 19