Yohane 18:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pilato ananena kwa iye, Coonadi nciani? Ndipo pamene adanena ici, anaturukiranso kwa Ayudawo, nanena nao, vine sindipeza konse cifukwa mwa iye.

Yohane 18

Yohane 18:35-40