Yohane 18:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Pilato anati kwa iwo, Mumtenge iye inu, ndi kumweruza iye monga mwa cilamulo canu. Ayuda anati kwa iye, Tiribe ulamuliro wakupha munthu ali yense;

Yohane 18

Yohane 18:25-33