Yohane 18:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Simoni Petro pokhala nalo lupanga, analisolola nakantha kapolo wa mkulu wa ansembe, namsenga khutu lace lamanja. Koma dzina lace la kapoloyo ndiye Malko.

Yohane 18

Yohane 18:9-12