Yohane 17:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma moyo wosatha ndi uwu, kuti akadziwe Inu Mulungu woona yekha, ndi Yesu Kristu amene munamtuma.

Yohane 17

Yohane 17:1-12