Yohane 17:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ine mwa iwo, ndi Inu mwa Ine, kuti akhale angwiro mwa mmodzi; kutr dziko lapansi lizindikire kuti Inu munandituma Ine, nimunawakonda iwo, monga momwe munakonda Ine,

Yohane 17

Yohane 17:18-26