Yohane 17:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti onse akakhale amodzi, monga Inu Atate mwa Ine, ndi Ine mwa Inu, kuti iwonso akakhale mwa Ife: kuti dziko lapansi likakhulupire kuti Inu munandituma Ine.

Yohane 17

Yohane 17:16-26