Yohane 17:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Monga momwe munandituma Ine ku dziko lapansi, Inenso ndinatuma iwo ku dziko lapansi,

Yohane 17

Yohane 17:16-26