Yohane 17:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Sindikhalanso m'dziko lapansi, koma iwo ali m'dziko lapansi, ndipo Ine ndidza kwa Inu. Atate. Woyera, sungani awa m'dzina lanu amene mwandipatsa Ine, kuti akhale mmodzi, monga Ife.

Yohane 17

Yohane 17:1-18