Yohane 16:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ndinena Ine coonadi ndi inu; kuyenera kwa inu kuti ndicoke Ine; pakuti ngati sindicoka, Nkhosweyo sadzadza kwa inu; koma ngati ndipita ndidzamtuma iye kwa inu.

Yohane 16

Yohane 16:3-14