Yohane 16:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma zinthu izi ndalankhula ndi inu kuti ikadza nthawi yao, mukakumbukire kuti ndinakuuzani. Koma izi sindinanena kwa inu kuyambira paciyambi, cifukwa ndinali pamodzi ndi inu.

Yohane 16

Yohane 16:1-12