Yohane 16:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zinthu izi ndalankhula ndi inu, kuti mwa Ine mukakhale nao mtendere. M'dziko lapansi mudzakhala naco cibvuto, koma limbikani mtima; ndalilaka dziko lapansi Ine.

Yohane 16

Yohane 16:32-33