Yohane 16:29-31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

29. Akuphunzira ace ananena, Onani, tsopano mulankhula zomveka, ndipo mulibe kunena ciphiphiritso,

30. Tsopano tidziwa kuti mudziwa zonse, ndipo mulibe kusowa kuti wina akafunse Inu; mwa ici tikhulupirira kuti munaturuka kwa Mulungu.

31. Yesu anayankha iwo, Kodi mukhulupirira tsopano?

Yohane 16