Yohane 16:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zinthu izi ndalankhula ndi inu m'mafanizo; ikudza nthawi imene sindidzalankhula ndi inu m'mafanizo, koma ndidzakulalikirani inu momveka za Atate.

Yohane 16

Yohane 16:24-28