Yohane 16:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo inu tsono muli naco cisoni tsopano lino, koma ndidzakuonaninso, ndipo mtima wanu udzakondwera, ndipo palibe wina adzacotsa kwa inu cimwemwe canu.

Yohane 16

Yohane 16:15-23