Yohane 16:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Indetu, indetu, ndinena ndi inu, kuti mudzalira ndi kubuma maliro inu, koma dziko lapansi lidzakondwera; mudzacita cisoni inu, koma cisoni canu cidzasandulika cimwemwe.

Yohane 16

Yohane 16:13-27