Yohane 16:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zinthu ziri zonse Atate ali nazo ndi zanga; cifukwa cace ndinati, kuti atenga za mwa Ine, nadzalalikira kwa inu.

Yohane 16

Yohane 16:13-22