Yohane 16:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Izi ndalankhula ndi inu kuti mungakhumudwitsidwe.

2. Adzakuturutsani m'masunagoge; koma ikudza nthawi imene yense wakupha inu adzayesa kuti atumikira Mulungu,

Yohane 16