Yohane 15:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ngati wina sakhala mwa Ine, watayika kunja monga nthambi, nafota; ndipo azisonkhanitsa nazitaya kumoto, nazitentha.

Yohane 15

Yohane 15:4-11