Yohane 15:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Khalani mwa Ine, ndi Ine mwa inu. Monga nthambi siingathe kubala cipatso pa yokha, ngati siikhala mwampesa; motere mulibe inunso ngati simukhala mwa Ine.

Yohane 15

Yohane 15:3-13