Yohane 15:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma pamene wafika Nkhoswe, amene Ine ndidzamtuma kwa inu kucokera kwa Atate, ndiye Mzimu wa coonadi, amene aturuka kwa Atate, Iyeyu adzandicitira Ine umboni.

Yohane 15

Yohane 15:23-27