Yohane 14:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mwamva kuti Ine ndinanena kwa inu, 6 Ndimuka, ndipo ndidza kwa inu. Mukadandikonda Ine, mukadakondwera kuti ndipita kwa Atate; 7 pakuti Atate ali wamkuru ndi Ine.

Yohane 14

Yohane 14:20-30