Yohane 14:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma 2 Nkhosweyo, Mzimu Woyera, amene Atate adzamtuma m'dzina langa, 3 Iyeyo adzaphunzitsa Inu zonse, nadzakumbutsa inu zinthu zonse zimene ndinanena kwa inu.

Yohane 14

Yohane 14:21-31