Yohane 14:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yudase, si Isikariote, ananena ndi iye, Ambuye, cacitika ciani kuti muziti mudzionetsa nokha kwa ife, koma si kwa dziko lapansi?

Yohane 14

Yohane 14:13-29