Yohane 14:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Katsala kanthawi, ndipo dziko lapansi silindionanso Ine; koma inu mundiona; popeza Ine ndiri ndi moyo inunso mudzakhala ndi moyo.

Yohane 14

Yohane 14:10-27