Yohane 14:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndiye Mzimu wa coonadi; amene dziko lapansi silingathe kumlandira, pakuti silimuona iye, kapena kumzindikira iye. Inu mumzindikira iye; cifukwa akhala ndi inu nadzakhala mwa inu.

Yohane 14

Yohane 14:15-24