Yohane 13:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pomwepo anathira madzi m'nsambidwe, nayamba kusambitsa mapazi a akuphunzira ace, ndi kuwapukuta ndi copukutira, cimene anadzimanga naco,

Yohane 13

Yohane 13:1-14