Yohane 13:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tiana, katsala kanthawi ndikhala ndi inu. Mudzandifunafuna Ine; ndipo monga ndinanena kwa Ayuda, kuti kumene ndinkako Ine, inu simungathe kudza, momwemo ndinena kwa inu tsopano.

Yohane 13

Yohane 13:25-38