Yohane 13:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yesu ananena naye, Amene anatha kusamba alibe kusowa koma kusamba mapazi, koma ayera monse: ndipo inu ndinu oyera, koma si nonse ai.

Yohane 13

Yohane 13:3-15