Yohane 12:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo khamu lalikuru la Ayuda Iinadziwa kuti ali pomwepo; ndipo anadza, si cifukwa: ca Yesu yekha, koma kuti adzaone Lazaro, amene adamuukitsa kwa akufa.

Yohane 12

Yohane 12:6-14