Yohane 12:50 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidziwa kuti lamulo lace liri moyo wosatha; cifukwa cace zimene ndilankhula, monga momwe Atate wanena ndi Ine, momwemo ndilankhula.

Yohane 12

Yohane 12:49-50