Yohane 12:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo khamulo linayankha iye, Tidamva ife m'cilamulo kuti Kristu akhala ku nthawi yonse; ndipo Inu munena bwanji, kuti Mwana wa munthu ayenera kukwezedwa? Mwana wa munthu amene ndani?

Yohane 12

Yohane 12:26-39