Yohane 12:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace Afarisi ananena wina ndi mnzace, Muona kuti simupindula kanthu konse; onani dziko litsata pambuyo pace pa iye.

Yohane 12

Yohane 12:11-29