Yohane 11:56 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo analikumfuna Yesu, nanena wina ndi mnzace poimirira iwo m'Kacisi, Muyesa bwanji inu, sadzadza kuphwando kodi?

Yohane 11

Yohane 11:49-57