Yohane 11:54 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace Yesu sanayandeyendanso poonekera mwa Ayuda, koma anacokapo kunka ku dziko loyandikira cipululu, kumudzi dzina lace Efraimu; nakhala komweko pamodzi ndi akuphunzira ace.

Yohane 11

Yohane 11:46-56