Yohane 11:51 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ici sananena kwa iye yekha; koma pokhala mkulu wa ansembe caka comweco ananenera kuti Yesu akadzafera mtunduwo;

Yohane 11

Yohane 11:44-56