Yohane 11:42 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ndadziwa Ine kuti mumandimva Ine nthawi zonse; koma cifukwa ca khamu la anthu alikuimirira pozungulira ndinanena ici, kuti akhulupire kuti Inu munandituma Ine.

Yohane 11

Yohane 11:36-44