Yohane 11:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Yesu pamene anamva, anati, Kudwala kumene sikuli kwa imfa, koma cifukwa ca ulemerero wa Mulungu, kuti Mwana wa Mulungu alemekezedwe nako.

Yohane 11

Yohane 11:1-14