Yohane 11:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yesu ananena, Cotsani mwala. Marita, mlongo wace wa womwalirayo, ananena ndi iye, Ambuye, adayamba kununkha: pakuti wagona masiku anai.

Yohane 11

Yohane 11:33-40