Yohane 10:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iyeyu, wapakhomo amtsegulira ndi nkhosa zimva mau ace; ndipo aitana nkhosa za iye yekha maina ao, nazitsogolera kunja.

Yohane 10

Yohane 10:1-8